Blog Detail

MBIRI YA MALEMU SR. MARY KIZITA JALASI – POOR CLARE

SISTER MARY KIZITA JALASI ANABADWA PA 27 JULY, 1944. IWO AMACHOKERA KU BALAKA.
SISTER MARY ANALOWA MNYUMBA YOBINDIKIRA YA POOR CLARES MCHAKA CHA 1963 NDIPO ANACHITA MALUMBIRO WOYAMBA PA 8 DECEMBER, 1966. MALUMBIRO OTSIRIZA ANACHITA MCHAKA CHA 1970.

SISTER MARY MMENE AMATISIYA PA 8 NOVEMBER, 2021 AKHALA MNYUMBA YOBINDIKIRA KWA ZAKA 58.

SISTER MARY AMAKHALA BWINO NDI AZIMAI ANZAWO.
AMAKONDA MAPEMPHERO KWAMBIRI
AMAPEKA NDI KUYIMBA NYIMBO
ANALI A MAI A CHIMWEMWE

MZIMU WAO UUSE NDI MTENDERE