CHIKONDWERERO CHA SILVER JUBILEE YA FR. KAPIRI (MZITHUNZI)
Mwambo wa nsembe ya Misa yokondwelera kuti bambo Peter Kapiri Mwale akwanitsa zaka 25 akutumikira ngati wa nsembe (1999 – 2024).
Mwambo wa nsembe ya Misayi unatsogoleredwa ndi ambuye George Desmond Tambala a Arkidayosizi ya Katolika ya Lilongwe pa 21 September 2024 ku Parishi ya St. Francis of Assisi, Kanengo.
Mwazina, bambo Kapiri anabwerezaso malonjezo awo a unsembe ndi kulonjeza kupitilira kutumikira mulungu mwa totomoyo.
Izi ndi zina mwa zithunzi zomwe Eric Norman Mkwaira wa Radio Alinafe anajambula pa mwambowu.
Vie all pictures here.