Amayi akatolika kuchokera mu Arkidayosizi ya Lilongwe alimbikitsidwa kupewa mchitidwe wochita zinthu zoipa pomwe akukhala moyo wawo wa tsiku ndi tsiku